Luka 22:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Yesu anauzanso ophunzirawo kuti: “Pamene ndinakutumizani opanda chikwama cha ndalama, thumba la chakudya kapena nsapato,+ kodi munasowa kanthu?” Iwo anati: “Ayi!”
35 Yesu anauzanso ophunzirawo kuti: “Pamene ndinakutumizani opanda chikwama cha ndalama, thumba la chakudya kapena nsapato,+ kodi munasowa kanthu?” Iwo anati: “Ayi!”