Luka 22:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Chifukwa ndikukuuzani kuti zimene zinalembedwa ziyenera kukwaniritsidwa mwa ine, zakuti, ‘Iye anaikidwa mʼgulu la anthu osamvera malamulo.’+ Zili choncho chifukwa zimene zinanenedwa zokhudza ine zikukwaniritsidwa.”+
37 Chifukwa ndikukuuzani kuti zimene zinalembedwa ziyenera kukwaniritsidwa mwa ine, zakuti, ‘Iye anaikidwa mʼgulu la anthu osamvera malamulo.’+ Zili choncho chifukwa zimene zinanenedwa zokhudza ine zikukwaniritsidwa.”+