Luka 22:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Atafika pamalowo anauza ophunzirawo kuti: “Pitirizani kupemphera kuti musalowe mʼmayesero.”+