-
Luka 22:41Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
41 Iye anachoka pamene panali ophunzirawo nʼkuyenda kamtunda, kutalika kwake ngati pamene pangagwere mwala munthu atauponya. Kumeneko anagwada nʼkuyamba kupemphera
-