Luka 22:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Atanyamuka pamene amapempherapo nʼkupita kwa ophunzira aja, anawapeza atagona chifukwa anali atafooka ndi chisoni.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:45 Nsanja ya Olonda,10/1/1990, tsa. 9
45 Atanyamuka pamene amapempherapo nʼkupita kwa ophunzira aja, anawapeza atagona chifukwa anali atafooka ndi chisoni.+