Luka 22:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Mawu adakali mʼkamwa, panafika gulu la anthu limodzi ndi Yudasi, mmodzi wa ophunzira 12 aja, akuwatsogolera. Ndiyeno Yudasi anapita pamene panali Yesu kuti akamukise.*+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:47 Yesu—Ndi Njira, tsa. 284 Nsanja ya Olonda,10/15/1990, tsa. 8
47 Mawu adakali mʼkamwa, panafika gulu la anthu limodzi ndi Yudasi, mmodzi wa ophunzira 12 aja, akuwatsogolera. Ndiyeno Yudasi anapita pamene panali Yesu kuti akamukise.*+