-
Luka 22:49Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
49 Anthu amene anali naye pafupi ataona zimene zinkachitika anati: “Ambuye, kodi tiwateme ndi lupanga?”