Luka 22:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Ndiyeno Yesu anafunsa ansembe aakulu, oyangʼanira kachisi ndi akulu amene anabwera kudzamugwira kuti: “Bwanji mwabwera ndi malupanga ndi zibonga ngati mukudzalimbana ndi wachifwamba?+
52 Ndiyeno Yesu anafunsa ansembe aakulu, oyangʼanira kachisi ndi akulu amene anabwera kudzamugwira kuti: “Bwanji mwabwera ndi malupanga ndi zibonga ngati mukudzalimbana ndi wachifwamba?+