Luka 22:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Zitatero anamugwira nʼkumutenga+ ndipo anakamulowetsa mʼnyumba ya mkulu wa ansembe. Koma Petulo ankawatsatira chapatali.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:54 Yesu—Ndi Njira, tsa. 288 Nsanja ya Olonda,11/15/1990, tsa. 8
54 Zitatero anamugwira nʼkumutenga+ ndipo anakamulowetsa mʼnyumba ya mkulu wa ansembe. Koma Petulo ankawatsatira chapatali.+