Luka 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako Pilato anauza ansembe aakulu ndi gulu la anthulo kuti: “Sindikupeza mlandu uliwonse mwa munthu uyu.”+
4 Kenako Pilato anauza ansembe aakulu ndi gulu la anthulo kuti: “Sindikupeza mlandu uliwonse mwa munthu uyu.”+