-
Luka 23:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Koma iwo anaumirira nʼkunena kuti: “Iyeyu akusokoneza anthu mwa kuphunzitsa mu Yudeya monse, kuyambira ku Galileya mpaka kudzafika kuno.”
-