Luka 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno atadziwa kuti akuchokera mʼchigawo chimene amalamulira Herode,+ anamutumiza kwa Herode, amenenso mʼmasiku amenewo anali mu Yerusalemu. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:7 Yesu—Ndi Njira, tsa. 292 Nsanja ya Olonda,12/15/1990, tsa. 8
7 Ndiyeno atadziwa kuti akuchokera mʼchigawo chimene amalamulira Herode,+ anamutumiza kwa Herode, amenenso mʼmasiku amenewo anali mu Yerusalemu.