Luka 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Herode ataona Yesu anasangalala kwambiri. Kwa nthawi yaitali ndithu ankafunitsitsa kuti aone Yesu chifukwa anali atamva zambiri zokhudza iye.+ Komanso ankayembekezera kuti aone chizindikiro chimene iye angachite. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:8 Yesu—Ndi Njira, tsa. 292 Nsanja ya Olonda,12/15/1990, tsa. 8
8 Herode ataona Yesu anasangalala kwambiri. Kwa nthawi yaitali ndithu ankafunitsitsa kuti aone Yesu chifukwa anali atamva zambiri zokhudza iye.+ Komanso ankayembekezera kuti aone chizindikiro chimene iye angachite.