Luka 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Herode limodzi ndi asilikali ake anamuchitira zachipongwe.+ Anamunyoza+ pomuveka chovala chokongola kwambiri, kenako anamutumizanso kwa Pilato.
11 Ndiyeno Herode limodzi ndi asilikali ake anamuchitira zachipongwe.+ Anamunyoza+ pomuveka chovala chokongola kwambiri, kenako anamutumizanso kwa Pilato.