Luka 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 nʼkuwauza kuti: “Inu mwabweretsa munthu uyu kwa ine ndi mlandu wakuti akulimbikitsa anthu kuukira. Koma mwaona nokha! Ine ndamufunsa pamaso panu ndipo sindinamupeze ndi chifukwa chomuimbira milandu imene mukumunenezayi.+
14 nʼkuwauza kuti: “Inu mwabweretsa munthu uyu kwa ine ndi mlandu wakuti akulimbikitsa anthu kuukira. Koma mwaona nokha! Ine ndamufunsa pamaso panu ndipo sindinamupeze ndi chifukwa chomuimbira milandu imene mukumunenezayi.+