-
Luka 23:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ndipotu ngakhale Herode sanamupeze ndi mlandu, nʼchifukwa chake wamubweza kwa ife. Ndithudi ameneyu sanachite chilichonse choyenera chilango cha imfa.
-