Luka 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma gulu lonse linafuula kuti: “Ameneyu muthane naye basi, koma ife mutimasulire Baraba!”+