-
Luka 23:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Anawafunsa kachitatu kuti: “Chifukwa chiyani? Kodi iyeyu walakwa chiyani? Ine sindinamupeze ndi chifukwa chilichonse chomuphera. Choncho ndimukwapula nʼkumumasula.”
-