Luka 23:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atamva zimenezi anamuumiriza mokweza mawu kuti Yesu aphedwe basi. Anthuwo ankafuula mwamphamvu moti Pilato anangololera.+
23 Atamva zimenezi anamuumiriza mokweza mawu kuti Yesu aphedwe basi. Anthuwo ankafuula mwamphamvu moti Pilato anangololera.+