-
Luka 23:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Iye anamasula munthu amene anthuwo ankafuna, amene anaikidwa mʼndende pa mlandu woukira boma komanso kupha munthu. Koma Yesu anamupereka mʼmanja mwawo kuti achite zimene ankafuna.
-