Luka 23:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamene ankapita naye, iwo anagwira Simoni wa ku Kurene, amene ankachokera kudera lakumidzi. Iwo anamusenzetsa mtengo wozunzikirapo* kuti aunyamule nʼkumatsatira pambuyo pa Yesu.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:26 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 296-297 Nsanja ya Olonda,7/15/1992, tsa. 6 Mawu a Mulungu, tsa. 96
26 Pamene ankapita naye, iwo anagwira Simoni wa ku Kurene, amene ankachokera kudera lakumidzi. Iwo anamusenzetsa mtengo wozunzikirapo* kuti aunyamule nʼkumatsatira pambuyo pa Yesu.+