-
Luka 23:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Gulu lalikulu la anthu linkamutsatira kuphatikizapo azimayi ambiri amene ankadziguguda pachifuwa chifukwa cha chisoni komanso kumulirira.
-