Luka 23:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Yesu anacheukira azimayiwo nʼkunena kuti: “Inu ana aakazi a Yerusalemu, siyani kundilirira. Koma mudzilirire nokha ndi ana anu.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:28 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 296-297 Nsanja ya Olonda,1/15/1991, tsa. 9
28 Yesu anacheukira azimayiwo nʼkunena kuti: “Inu ana aakazi a Yerusalemu, siyani kundilirira. Koma mudzilirire nokha ndi ana anu.+