Luka 23:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mʼmasiku amenewo iwo adzayamba kuuza mapiri kuti, ‘Tigwereni!’ ndipo adzauza mapiri angʼonoangʼono kuti, ‘Tikwirireni!’+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:30 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 112
30 Mʼmasiku amenewo iwo adzayamba kuuza mapiri kuti, ‘Tigwereni!’ ndipo adzauza mapiri angʼonoangʼono kuti, ‘Tikwirireni!’+