Luka 23:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndiyeno atafika pamalo otchedwa Chibade,+ anamukhomerera pamtengo limodzi ndi zigawenga zija. Mmodzi anamupachika kudzanja lake lamanja ndipo wina anali kumanzere kwake.+
33 Ndiyeno atafika pamalo otchedwa Chibade,+ anamukhomerera pamtengo limodzi ndi zigawenga zija. Mmodzi anamupachika kudzanja lake lamanja ndipo wina anali kumanzere kwake.+