-
Luka 23:40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
40 Poyankha mnzake uja anamudzudzula kuti: “Kodi iwe sukuopa Mulungu poona kuti nawenso ukulandira chilango chofanana ndi cha munthu ameneyu?
-