-
Luka 23:41Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
41 Ifetu mpake kulangidwa chonchi, chifukwa tikulandira zimene timayenera kulandira mogwirizana ndi zimene tinachita. Koma munthu uyu sanalakwe chilichonse.”
-