-
Luka 23:48Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
48 Anthu onse amene anasonkhana kumeneko kudzaonerera zimene zinkachitikazo, ataona zonse zimene zinachitika, anabwerera kwawo akudziguguda pachifuwa.
-