-
Luka 23:51Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
51 (Iye sanavomereze chiwembu chawo komanso zimene anachita.) Yosefe anali wochokera ku Arimateya, mzinda wa Ayudeya ndipo ankayembekezera Ufumu wa Mulungu.
-