Luka 23:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Koma azimayi amene anabwera limodzi ndi Yesu kuchokera ku Galileya, anamutsatira ndipo anaona mandawo* komanso mmene mtembo wakewo anauikira.+
55 Koma azimayi amene anabwera limodzi ndi Yesu kuchokera ku Galileya, anamutsatira ndipo anaona mandawo* komanso mmene mtembo wakewo anauikira.+