Luka 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma pa tsiku loyamba la mlungu, azimayi aja analawirira mʼmawa kwambiri kupita kumandako,* atatenga zonunkhira zimene anakonza zija.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:1 Nsanja ya Olonda,3/1/2013, tsa. 83/1/1991, tsa. 9
24 Koma pa tsiku loyamba la mlungu, azimayi aja analawirira mʼmawa kwambiri kupita kumandako,* atatenga zonunkhira zimene anakonza zija.+