Luka 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Azimayiwo anagwidwa ndi mantha ndipo anaweramira pansi. Ndiyeno amunawo anawafunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukufunafuna munthu wamoyo pakati pa anthu akufa?+
5 Azimayiwo anagwidwa ndi mantha ndipo anaweramira pansi. Ndiyeno amunawo anawafunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani mukufunafuna munthu wamoyo pakati pa anthu akufa?+