Luka 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Petulo ananyamuka nʼkuthamangira kumandako,* ndipo atasuzumira mkati, anangoona nsalu zokha. Choncho anachoka ali wodabwa kwambiri ndi zimene zinachitikazo.
12 Koma Petulo ananyamuka nʼkuthamangira kumandako,* ndipo atasuzumira mkati, anangoona nsalu zokha. Choncho anachoka ali wodabwa kwambiri ndi zimene zinachitikazo.