-
Luka 24:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Iye anawafunsa kuti: “Kodi ndi nkhani zotani zimene mukukambirana mukuyenda pamsewu pano?” Iwo anangoima chilili akuoneka achisoni.
-