Luka 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Poyankha, mmodzi wa iwo dzina lake Keleopa, anamufunsa kuti: “Kodi iwe ukukhala wekhawekha mʼYerusalemu monga mlendo,* moti sukudziwa zinthu zimene zachitika mmenemo mʼmasiku amenewa?”
18 Poyankha, mmodzi wa iwo dzina lake Keleopa, anamufunsa kuti: “Kodi iwe ukukhala wekhawekha mʼYerusalemu monga mlendo,* moti sukudziwa zinthu zimene zachitika mmenemo mʼmasiku amenewa?”