Luka 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Komanso zokhudza mmene ansembe athu aakulu ndi olamulira anamuperekera kwa anthu amene anamuweruza kuti aphedwe ndipo anamukhomerera pamtengo.+
20 Komanso zokhudza mmene ansembe athu aakulu ndi olamulira anamuperekera kwa anthu amene anamuweruza kuti aphedwe ndipo anamukhomerera pamtengo.+