Luka 24:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Atatero anayamba kuwatanthauzira zinthu zokhudza iyeyo mʼMalemba onse, kuyambira ndi Zolemba za Mose komanso zonse zimene aneneri analemba.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:27 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 18
27 Atatero anayamba kuwatanthauzira zinthu zokhudza iyeyo mʼMalemba onse, kuyambira ndi Zolemba za Mose komanso zonse zimene aneneri analemba.+