Luka 24:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamene ankadya nawo chakudya,* anatenga mkate nʼkuudalitsa, kenako anaunyemanyema nʼkuyamba kuwagawira.+
30 Pamene ankadya nawo chakudya,* anatenga mkate nʼkuudalitsa, kenako anaunyemanyema nʼkuyamba kuwagawira.+