-
Luka 24:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Pa ola lomwelo ananyamuka nʼkubwerera ku Yerusalemu. Kumeneko anakapeza ophunzira 11 aja komanso anthu ena amene anasonkhana nawo pamodzi.
-