Luka 24:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Akulankhula choncho, Yesu anaimirira pakati pawo nʼkuwauza kuti: “Mtendere ukhale nanu.”+