-
Luka 24:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Onani manja ndi mapazi angawa, mutsimikize kuti ndine ndithu. Ndikhudzeni muone, chifukwa mzimu ulibe mnofu ndi mafupa ngati anga amene mukuwaonawa.”
-