-
Luka 24:41Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
41 Koma popeza iwo sankakhulupirirabe chifukwa cha chimwemwe ndi kudabwa, iye anawafunsa kuti: “Kodi muli ndi chakudya chilichonse pano?”
-