Luka 24:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 ndipo mʼdzina lake, uthenga woti anthu alape machimo awo+ kuti akhululukidwe udzalalikidwa kwa anthu a mitundu yonse,+ kuyambira ku Yerusalemu.+
47 ndipo mʼdzina lake, uthenga woti anthu alape machimo awo+ kuti akhululukidwe udzalalikidwa kwa anthu a mitundu yonse,+ kuyambira ku Yerusalemu.+