Luka 24:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Pamene ankawadalitsa, analekana nawo ndipo Mulungu anamutenga kupita naye kumwamba.+