Yohane 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komabe onse amene anamulandira, anawapatsa mphamvu kuti akhale ana a Mulungu,+ chifukwa choti ankakhulupirira dzina lake.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:12 Nsanja ya Olonda,4/1/2001, tsa. 54/1/1993, tsa. 12 Kukambitsirana, ptsa. 158, 206
12 Komabe onse amene anamulandira, anawapatsa mphamvu kuti akhale ana a Mulungu,+ chifukwa choti ankakhulupirira dzina lake.+