Yohane 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye anati: “Ndine mawu a winawake amene akufuula mʼchipululu kuti, ‘Wongolani njira ya Yehova,’*+ monga mmene mneneri Yesaya ananenera.”+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:23 Yesaya 1, ptsa. 399-401 Kukambitsirana, tsa. 401
23 Iye anati: “Ndine mawu a winawake amene akufuula mʼchipululu kuti, ‘Wongolani njira ya Yehova,’*+ monga mmene mneneri Yesaya ananenera.”+