Yohane 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Zinthu zimenezi zinachitikira ku Betaniya, kutsidya la Yorodano, kumene Yohane ankabatiza anthu.+