Yohane 1:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Iye anawauza kuti: “Tiyeni mukaoneko.” Choncho anapita kukaona kumene ankakhala ndipo anakhala naye tsiku limenelo. Apa nʼkuti nthawi ili cha mʼma 4 koloko madzulo.* Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:39 Yesu—Ndi Njira, tsa. 38
39 Iye anawauza kuti: “Tiyeni mukaoneko.” Choncho anapita kukaona kumene ankakhala ndipo anakhala naye tsiku limenelo. Apa nʼkuti nthawi ili cha mʼma 4 koloko madzulo.*