Yohane 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano Pasika+ wa Ayuda anali atayandikira, choncho Yesu ananyamuka nʼkupita ku Yerusalemu.