Yohane 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho anapanga chikwapu chazingwe nʼkuthamangitsa onse amene anali ndi nkhosa komanso ngʼombe mʼkachisimo. Anakhuthula makobidi a anthu osintha ndalama nʼkugubuduza matebulo awo.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:15 Yesu—Ndi Njira, tsa. 43 Nsanja ya Olonda,6/15/1987, ptsa. 12-13
15 Choncho anapanga chikwapu chazingwe nʼkuthamangitsa onse amene anali ndi nkhosa komanso ngʼombe mʼkachisimo. Anakhuthula makobidi a anthu osintha ndalama nʼkugubuduza matebulo awo.+